Frequently Asked Questions
Frequently Asked Questions (FAQ)
1. What is the entire delivery process?
Read our Order Guidance to understand the entire online delivery service, You can also Contact Us to ask any questions that you may have.
1. Kodi ndondomeko yonse ya kutumiza katundu imakhala bwanji?
Werengani Order Guidance yathu kuti mumvetse bwino za ntchito yathu yonse ya kutumiza katundu pa intaneti. Muthanso kutilankhula ngati muli ndi mafunso ena aliwonse.
2. How long does it take for my goods to be delivered?
You can choose Schedule your Delivery in any of the following delivery slots:
- We're open from 9am to 5pm
- Next-Day, Early Slot (9AM-1PM)
- Next-Day, Afternoon Slot (1PM-5PM)
Please note that delivery times may vary based on your location and the availability of the items you ordered.
2. Zimatenga nthawi yaitali bwanji kuti katundu wanga abwere?
Mutha kusankha nthawi yomwe mukufuna katundu wanu atumizidwe kuchokera m’malo otsatirawa:
- Tili otseguka kuyambira 9am mpaka 5pm
- Tsiku Lotsatira, Gawo Loyambirira (9AM–1PM)
- Tsiku Lotsatira, Gawo Lachiwiri (1PM–5PM)
Chonde dziwani kuti nthawi yotumizira imasiyana malinga ndi komwe muli ndi kupezeka kwa zinthu zomwe mwalamula.
3. What is the minimum basket size?
To place an order, there is a minimum basket size of MK30,000. This ensures we can efficiently manage and deliver your orders.
3. Kodi ndalama zochepa zoyenera kuti ndiyitanitse katundu ndi zingati?
Kuti muyitanitse katundu, muyenera kukhala ndi ndalama zosachepera MK30,000. Izi zimathandiza kuti titumize bwino komanso mwadongosolo.
4. How can I track my order?
You can track your order using the tracking number provided in your order confirmation email. Simply call us to hear from us the latest status of your delivery at +265 997 65 07 33/+265 982 74 08 96
4. Ndingatsatire bwanji katundu wanga?
Mungatsatire katundu wanu pogwiritsa ntchito nambala yotsatira (tracking number) yomwe imatumizidwa pa imelo ya chitsimikizo cha dongosolo lanu. Ingotipatsani foni kuti mumve momwe katundu wanu alili pa: +265 997 65 07 33 / +265 982 74 08 96
5. How does payment work?
We offer various payment options to make your shopping experience as convenient as possible:
- Mobile Payments
- Cash on Delivery
Read our Payments Policy to get more information regarding payments.
5. Kodi malipiro amachitika bwanji?
Timapereka njira zosiyanasiyana zolipirira kuti kugula kwanu kukhale kosavuta kwambiri:
Malipiro a pa foni (Mobile Payments)
Kulipira pakupeleka katundu (Cash on Delivery)
Werengani Payments Policy yathu kuti mumve zambiri za malipiro.
6. What if I have an issue with my order?
If you encounter any issues with your order, please Contact Us immediately, or visit our customer service desk at Sana Megastore, Lilongwe.
We are committed to resolving any issues promptly and ensuring your satisfaction.
6. Ndingatani ngati ndili ndi vuto pa dongosolo langa?
Ngati mwakumana ndi vuto pa dongosolo lanu, tilankhuleni nthawi yomweyo, kapena pitani ku desiki lathu la makasitomala ku Sana Megastore, Lilongwe.
Tadzipereka kuthetsa vutolo mwachangu komanso kutsimikizira kuti mukukhutitsidwa.